![]() |
Malavi Milli Marşı - Malavi Ulusal Marşı |
![]() |
![]() |
#1 |
Prof. Dr. Sinsi
|
![]() Malavi Milli Marşı - Malavi Ulusal MarşıMalavi Milli Marşı Sözleri Malavi Ulusal Marşı Ülkelerin Milli Marşı Sözleri Malavi Ülkesinin Milli Marşı Sözleri Mlungu dalitsani Malawi, Mumsunge m'mtendere ![]() Gonjetsani adani onse, Njala, nthenda, nsanje ![]() Lunzitsani mitima yathu, Kuti tisaope ![]() Mdalitse Mtsogo leri na fe, Ndi Mai Malawi ![]() Malawi ndziko lokongola, La chonde ndi ufulu, Nyanja ndi mphepo ya m'mapiri, Ndithudi tadala ![]() Zigwa, mapiri, nthaka, dzinthu, N'mphatso zaulere ![]() Nkhalango, madambo abwino ![]() Ngwokoma Malawi ![]() O! Ufulu tigwirizane, Kukweza Malawi ![]() Ndi chikondi, khama, kumvera, Timutumikire ![]() Pa nkhondo nkana pa mtendere, Cholinga n'chimodzi ![]() Mai, bambo, tidzipereke, Pokweza Malawi ![]() |
![]() |
![]() |
|